Organised Family – Loadshedding Lyrics (Ft. Yo Maps)

Organised Family
Orga Rex 1 my younger brother
The music teacher is here
Our electrical engineer
Kent, me on the deck [?]

[Chorus]
Sinifuna vama loadshedding ma blackouts
Oh oh mu chikondi chatu
Ichi
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Sinifuna vama loadshedding ma blackouts
Oh oh mu chikondi chatu
Ichi
Ndiwe weka baby

Get 1500 Pounds and 150 Free Spins On 1xbet Casino - Ulwimbo.com

Chikondi chatu chizi yaka-yaka pali ponse
Ntawi zonse ku shiner
Mmm chalo changa ichi
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Chikondi chatu chizi yaka-yaka pal ponse
Ntawi zonse ku shiner
Ichi mmm chalo changa

[Verse 1]
Ona baby
Ndiwe candle yanga
Malasha mu moyo wanga
Ah moyo wanga

Olo bakambe nimafuna baby you
Ku mutima nima kamba baby boo
Nifuna nikule chabe with you
Ndiwe weka baby

Konse tiza limba
Tizakwanisa na futi
Ndiwe nimafuna lyonse pa duty
Baby ndiwe chabe mutima wanga
Mmm chalo changa

[Chorus]
Sinifuna vama loadshedding ma blackouts
Oh oh mu chikondi chatu
Ichi
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Sinifuna vama loadshedding ma blackouts
Oh oh mu chikondi chatu
Ichi
Ndiwe weka baby

Chikondi chatu chizi yaka-yaka pali ponse
Ntawi zonse ku shiner
Mmm chalo changa ichi
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Chikondi chatu chizi yaka-yaka pali ponse
Ntawi zonse ku shiner
Ichi mmm chalo changa

[Verse 2]
Chikondi cha generator
Fuel ikasila
Malaiti yamazima

Chikondi chama gesi
Yaja ya ku pole (ya ku pole)
Boma imazimya ikafuna pali ponse

But chikondi chatu my baby
Chichoke direct from the sun
Natural love (solar energy)

[Chorus]
Sinifuna vama loadshedding ma blackouts
Oh oh mu chikondi chatu
Ichi
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Sinifuna vama loadshedding ma blackouts
Oh oh mu chikondi chatu
Ichi
Ndiwe weka baby

Chikondi chatu chizi yaka-yaka pali ponse
Ntawi zonse ku shiner
Mmm chalo changa ichi
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Chikondi chatu chizi yaka-yaka pali ponse
Ntawi zonse ku shiner
Ichi mmm chalo changa

[Bridge]
Olo vikose tiza limba
Tiza kwanisa na futi
Ndiwe nimafuna lyonse pa duty
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Light ya mu mutima wanga
(Ya mu mutima wanga)
Mmm chalo changa
Direct from the sun
Natural love (solar energy)

[Chorus]
Sinifuna vama loadshedding ma blackouts
Oh oh mu chikondi chatu
Ichi
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Sinifuna vama loadshedding ma blackouts
Oh oh mu chikondi chatu
Ichi
Ndiwe weka baby

Chikondi chatu chizi yaka-yaka pali ponse
Ntawi zonse ku shiner
Mmm chalo changa ichi
Baby ndiwe chabe mutima wanga

Chikondi chatu chizi yaka-yaka pali ponse
Ntawi zonse ku shiner
Ichi mmm chalo changa

Share this
Subscribe
Notify of
guest

0 Comments
Most Upvoted
Newest Oldest
Inline Feedbacks
View all comments