T-Sean – Nitumile Lyrics

[Verse 1]
Sindiwe
We unakamba
Ati ufunako space yayi ndine
Ndine
Ndine
Ndine

Ndine nenzo meka pe wenzo funa
Vintu visebenze
Ndine
Ndine

Sininga dabwe kunvela
Kuti unapeza kale wina
It was my fault
I let you go

[Chorus]
Baby please ngati unimvela
Niku pempa
Ngati ukachili single monga ine
Nitumile

Life si iwama kulibe iwe
‘Cause life si iwama kulibe iwe

Baby please ngati unimvela
Niku pempa
Ngati ukachili single monga ine
Nitumile

‘Cause life si iwama kulibe iwe
Life si iwama kulibe iwe

[Verse 2]
Lelo niziba uzanvela nyimbo zambili
On the radio
This is not just another love song
This is me saying nakuyewa
Right now

Oh baby si nina chaye move on
Nenzo yembekeza iwe
Ninga nkale nayi taya
Koma mu mutima muli weo
Nenze chipuba
I let you go

[Chorus]
Baby please ngati unimvela
Niku pempa
Ngati ukachili single monga ine
Nitumile

Life si iwama kulibe iwe
‘Cause life si iwama kulibe iwe

Baby please ngati unimvela
Niku pempa
Ngati ukachili single monga ine
Nitumile

‘Cause life si iwama kulibe iwe
Life si iwama kulibe iwe
‘Cause life si iwama kulibe iwe
Life si iwama kulibe iwe

Share this
Subscribe
Notify of
guest

0 Comments
Most Upvoted
Newest Oldest
Inline Feedbacks
View all comments