Namadingo – Lalala (Ft. Tay Grin)

La La La Lyrics by Namadingo (Ft. Tay Grin) | Ulwimbo.com

Namadingo – Lalala Lyrics (Ft. Tay Grin)

[Intro – Namadingo]
Alipo alipo ondi-
Alipo alipo ondi-

[Verse 1 – Namadingo]
Alipo ondidelera
M’maso mwawo ndimachepera
Akuti nyimbo zanga samvera
Ndi-ndi, ndipo sine oyenera

Kumanditchula dokotala
Ndilibe PhD papepala
Angondipatsa udokotalawu
Nde wina akamva Doc sasangalala

Eti mpaka kunditchula kuti wamsala
Ndingothokoza Mulungu oyera amandikondera
Madalitso akubwera tikulemera
Namadingo most followed mumfuse [pa chart?]

[Chorus – Namadingo]
Adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)

[Verse 2 – Tay Grin]
Rrr-rah, dats de fire dere

Mfumu yazinyawu (ija)
Flow so sick I need a doctor to feature
I am not an average joe
They pay me what you make in a year for a show

In a deck of cards I’m the jokеr
I’m the extremе opposite of mediocre
Simungamake ndine messi pa soccer
Grin ndi messi pa soccer (yeah)

Too many international awards
I’m representing Malawi, your bro
Doing this till I grow old
(Nanga Time Square?)
Ndili pa billboard

[Chorus – Namadingo]
Ena adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)

Ena adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)

[Verse 2]
[Namadingo]
Muliponso ena all over the world
Mumadeleledwa kuchepetsedwa

[Tay Grin]
If you visualize it, you’re bound to do it
Life’s a jungle, me I rumble through it
If I can do it, y’all can do it
From the frontline, put your back into it

[Chorus – Namadingo]
Ena adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)

Ena adzavomeleza too late (pano iwo ndi lalala)
Kuti mwana uja ndi dolo (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)
Koma too late, too late, too late (pano iwo ndi lalala)

[Outro: Tay Grin]
Joe Gwaladi aseh uli bho?

Share this
Subscribe
Notify of
guest

0 Comments
Most Upvoted
Newest Oldest
Inline Feedbacks
View all comments