Mitengeli – Ndalama Lyrics (Ft. Namadingo)

Namadingo

Hmmm djeee ndalama ndalama
Money ikulamulira dziko
Mitengeli mwawerenga mawu
Awuzeni anthu

(Ati mwawerengaaaah)
Ndawerenga baibulo pena pake aaah
(Pena pake baibulo aah)
Zoipa zawo zamatsiku osiliza
(Anthu waaaaaah aah)
Anthu azakhala ozikonda okha

Get 1500 Pounds and 150 Free Spins On 1xbet Casino - Ulwimbo.com

(Komanso)
Komanso okonda ndalama
(Nde imbani ndi zida)
Ndawerenga baibulo pena pake aaah
(Pena pake baibulo ooh ooh)
Uchabechabe wachuma chapadziko aaah
(Iiyiiiih iih iiih)

Zimbili ndi njenjete zimaononga aaah
Sizingagulenso moyo

(Ooooh zaulendo uno)
Zaulendo uno zokwanilitsa malemba
(Zokwanilitsa malemba)
Zaulendo uno

(Amene ali ndi makwacha)
Amene ali ndi ndalama ulemu umawalondora
(Eeeeeeh eh eeh)
Zaulendo uno

(Amene alibe kanthu)
Amene alibe ndalama kumtenga ngati kachitsotso
(Mamamaah aaah aah)
Zaulendo uno

(Amene ali ndi ndalama)
Amene ali ndi ndalama milandu imawakomera
(Oooh ooh aaah)
Zaulendo uno

Share this
Subscribe
Notify of
guest

0 Comments
Most Upvoted
Newest Oldest
Inline Feedbacks
View all comments