Namadingo – Msati Mseke

Namadingo - Msati Mseke Lyrics - Ulwimbo.com
Msati Mseke Lyrics by Namadingo | Ulwimbo.com

Namadingo – Msati Mseke Lyrics

[Verse 1]
Msati mseke akadzola matope pepepe pepepe
Atavala chigoba choseketsa kunkhope pepe pepepe
Amathamangitsa mpaka wina atope pepe pepepe
Nkumukwapula mpaka wina pepepe pepepe

Ndalama yake awafupe pepe pepepe
Amasamba kudambo osati pampope pepe pepepe
Amati iwo nvilombo nvilombo nvilombo nvilombo
Napepepe

[Chorus]
Koma onsewo baibulo liti awafuna
Awafuna a-a awafuna
Eee awafuna a-a awafuna
Abwele avinile iyeyo awafuna a-a-a-a-a-a-a-a-a

Koma onsewa Baibulo liti awaitana
Awaita-ana awayitana
Awaita-ana awayitana
Abwele avinile iyeyo
Awaita-a-a-a-a-a-a-a-a-na

[Verse 2]
Msati mdabwe mkaona asilikali lili lililili
Atavala zawo koma zaasilikali lili lililili
Nsapato zawo atapolisha phuli phuli lililili
Akuvina monyada koma cham’mbali mbali lili lililili

Matupi awo atayaka ngati moto kubuka
Ngati moto kubuka liiiiii lililili
Pang’ono pang’ono dansi nkumakolela
Ngati ndi mlili lili
Sangavine yekha amavina kagulu ambili lilili

[Chorus]
Koma onsewo baibulo liti awafuna
Awafuna a-a awafuna
Eee awafuna a-a awafuna
Abwele avinile iyeyo awafuna a-a-a-a-a-a-a-a-a

Koma onsewa Baibulo liti awaitana
Awaita-ana awayitana
Awaita-ana awayitana
Abwele avinile iyeyo
Awaita-a-a-a-a-a-a-a-a-na

[Verse 3]
Msati mdabwe mkaona atchenetsetsa
Tsatsa tsatsatsatsa
Kabudula ndimalaya zoyeletsetsa
Tsatsa tsatsatsatsatsa

Stonkeni kampango koyeletsetsa
Tsa tsatsa tsatsatsatsa
Amavina monyang’wa koma monyang’witsitsa
Tsatsa tsatsatsatsa

Amamwetulila ngati akujambulitsa
Tsatsa tsatsatsatsa
Eh sungati ubele olo utayang’anitsitsa tsatsatsatsa
Koma sungati uvine olo atakuphuzintsa tsatsatsatsa

Koma Yehova baibulo lati mtifuna
Mtifuna a-a mtifuna
Ee mtifuna a-a mtifuna a Tibwele tivinile inuyo
Mtifuna aaaaaa mmm mm
Ati koma inu Yesu baibulo lati mtikonda
Ee mtikonda a-a mtikonda eee mtikonda mmm mtikonda

Share this
Subscribe
Notify of
guest
0 Comments
Inline Feedbacks
View all comments